2 Samueli 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo anthu onse a Isiraeli anayamba kuchoka kwa Davide ndi kutsatira Sheba mwana wa Bikiri.+ Koma anthu a ku Yuda, kuyambira ku Yorodano mpaka ku Yerusalemu anamamatira mfumu yawo.+
2 Pamenepo anthu onse a Isiraeli anayamba kuchoka kwa Davide ndi kutsatira Sheba mwana wa Bikiri.+ Koma anthu a ku Yuda, kuyambira ku Yorodano mpaka ku Yerusalemu anamamatira mfumu yawo.+