2 Samueli 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno mfumu inayamba kubwerera kwawo ndipo inafika ku Yorodano. Pamenepo anthu a Yuda anafika ku Giligala+ kuti apite kukakumana ndi mfumu ndi kuiperekeza pamene inali kuwoloka mtsinje wa Yorodano. 2 Samueli 19:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Pamenepo anthu a ku Yuda anayankha anthu a ku Isiraeli kuti: “Chifukwa chakuti mfumuyi ndi wachibale wathu wapafupi.+ N’chifukwa chiyani inu mwakwiya nazo zimenezi? Kodi ife tadya zinthu zilizonse za mfumu kapena kulandira mphatso?”
15 Ndiyeno mfumu inayamba kubwerera kwawo ndipo inafika ku Yorodano. Pamenepo anthu a Yuda anafika ku Giligala+ kuti apite kukakumana ndi mfumu ndi kuiperekeza pamene inali kuwoloka mtsinje wa Yorodano.
42 Pamenepo anthu a ku Yuda anayankha anthu a ku Isiraeli kuti: “Chifukwa chakuti mfumuyi ndi wachibale wathu wapafupi.+ N’chifukwa chiyani inu mwakwiya nazo zimenezi? Kodi ife tadya zinthu zilizonse za mfumu kapena kulandira mphatso?”