Yoswa 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndachotsa chitonzo cha Iguputo pa inu.”+ Chotero malowo anayamba kuwatchula kuti Giligala,+ kufikira lero. 1 Samueli 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Samueli anauza anthuwo kuti: “Tiyeni tipite ku Giligala+ kuti tikachitenso mwambo wolonga mfumu.”+
9 Kenako Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndachotsa chitonzo cha Iguputo pa inu.”+ Chotero malowo anayamba kuwatchula kuti Giligala,+ kufikira lero.
14 Kenako Samueli anauza anthuwo kuti: “Tiyeni tipite ku Giligala+ kuti tikachitenso mwambo wolonga mfumu.”+