Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Rute 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndipo kudzera mwa ana amene Yehova adzakupatsa kwa mtsikanayu,+ nyumba yako ikhale ngati nyumba ya Perezi, amene Tamara anaberekera Yuda.”+

  • Rute 4:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Obedi anabereka Jese,+ ndipo Jese anabereka Davide.+

  • 2 Samueli 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako amuna a ku Yuda+ anabwera ndi kudzoza+ Davide kumeneko kukhala mfumu ya nyumba ya Yuda.+

      Ndiyeno anthu anauza Davide kuti: “Anthu a ku Yabesi-giliyadi ndi amene anaika Sauli m’manda.”

  • Salimo 78:68
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 68 Koma anasankha fuko la Yuda,+

      Phiri la Ziyoni limene analikonda.+

  • Mateyu 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Yuda anabereka Perezi+ ndi Zera, ndipo mayi awo anali Tamara.

      Perezi anabereka Hezironi.+

      Hezironi anabereka Ramu.+

  • Mateyu 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Jese anabereka mfumu+ Davide.+

       Davide anabereka Solomo,+ yemwe mayi ake anali mkazi wa Uriya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena