1 Mbiri 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana a Shela+ mwana wa Yuda anali Ere bambo wa Leka, Laada bambo wa Maresha, ndi mabanja a nyumba ya anthu ogwira ntchito yopanga nsalu zabwino kwambiri,+ a nyumba ya Asibeya,
21 Ana a Shela+ mwana wa Yuda anali Ere bambo wa Leka, Laada bambo wa Maresha, ndi mabanja a nyumba ya anthu ogwira ntchito yopanga nsalu zabwino kwambiri,+ a nyumba ya Asibeya,