1 Mbiri 6:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Otsatirawa ndiwo malo amene ankakhala ana a Aroni a m’banja la Akohati,+ m’misasa yawo yokhala ndi mipanda m’madera awo,+ chifukwa maere anagwera iwowo:
54 Otsatirawa ndiwo malo amene ankakhala ana a Aroni a m’banja la Akohati,+ m’misasa yawo yokhala ndi mipanda m’madera awo,+ chifukwa maere anagwera iwowo: