1 Mbiri 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atsogoleriwa anathandiza Davide kulimbana ndi gulu la achifwamba,+ chifukwa atsogoleri onsewa anali amuna amphamvu+ ndi olimba mtima, ndipo anakhala atsogoleri a asilikali.
21 Atsogoleriwa anathandiza Davide kulimbana ndi gulu la achifwamba,+ chifukwa atsogoleri onsewa anali amuna amphamvu+ ndi olimba mtima, ndipo anakhala atsogoleri a asilikali.