1 Mbiri 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 A fuko la Benjamini,+ abale ake a Sauli,+ analipo 3,000. Kufikira pa nthawiyo, ambiri mwa anthu a fukolo, anali kulondera mosamala nyumba ya Sauli.
29 A fuko la Benjamini,+ abale ake a Sauli,+ analipo 3,000. Kufikira pa nthawiyo, ambiri mwa anthu a fukolo, anali kulondera mosamala nyumba ya Sauli.