1 Mbiri 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Benjamini+ anabereka Bela+ mwana wake woyamba, wachiwiri anali Asibeli,+ wachitatu anali Ahara,+ 1 Mbiri 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amuna onyamula mauta amenewa, ankatha kugwiritsa ntchito mkono wamanja ndi wamanzere+ kuponyera miyala+ kapena kuponyera mivi+ pa uta.+ Amenewa anali abale ake a Sauli wa fuko la Benjamini.
2 Amuna onyamula mauta amenewa, ankatha kugwiritsa ntchito mkono wamanja ndi wamanzere+ kuponyera miyala+ kapena kuponyera mivi+ pa uta.+ Amenewa anali abale ake a Sauli wa fuko la Benjamini.