1 Mbiri 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero, Davide anasonkhanitsa+ Aisiraeli onse kuchokera kumtsinje wa Iguputo+ mpaka kukafika polowera ku Hamati,+ kuti akatenge likasa+ la Mulungu woona ku Kiriyati-yearimu.+ 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:5 Nsanja ya Olonda,10/1/2005, ptsa. 10-11
5 Chotero, Davide anasonkhanitsa+ Aisiraeli onse kuchokera kumtsinje wa Iguputo+ mpaka kukafika polowera ku Hamati,+ kuti akatenge likasa+ la Mulungu woona ku Kiriyati-yearimu.+