1 Mbiri 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Afilisiti anamva kuti Davide amudzoza kukhala mfumu ya Isiraeli yense.+ Choncho Afilisiti onse anabwera kudzafunafuna Davide.+ Davide atamva zimenezi, anapita kukamenyana nawo.
8 Tsopano Afilisiti anamva kuti Davide amudzoza kukhala mfumu ya Isiraeli yense.+ Choncho Afilisiti onse anabwera kudzafunafuna Davide.+ Davide atamva zimenezi, anapita kukamenyana nawo.