1 Mbiri 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Afilisitiwo anafika ndi kuyamba kufunkha m’chigwa cha Arefai.+