2 Samueli 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Afilisitiwo anafika ndi kuyamba kuyendayenda m’chigwa cha Arefai.+ 2 Samueli 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Patapita nthawi, Afilisiti aja anabweranso+ ndi kuyamba kuyendayenda m’chigwa cha Arefai.+ 2 Samueli 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno pa nthawi yokolola, atatu mwa atsogoleri 30+ anapita kwa Davide kuphanga la Adulamu.+ Apa n’kuti Afilisiti atamanga msasa wa mahema m’chigwa cha Arefai.+
13 Ndiyeno pa nthawi yokolola, atatu mwa atsogoleri 30+ anapita kwa Davide kuphanga la Adulamu.+ Apa n’kuti Afilisiti atamanga msasa wa mahema m’chigwa cha Arefai.+