Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 15:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kuchokera pamenepo, anapitirira mpaka kuchigwa cha mwana wa Hinomu,+ kumalo otsetsereka otchedwa Yebusi+ kum’mwera, kutanthauza Yerusalemu.+ Anapitirirabe mpaka pamwamba pa phiri loyang’anizana ndi chigwa cha Hinomu, limene lili kumadzulo kwa chigwacho. Phirilo lili kumpoto kwa chigwa cha Arefai,+ kumapeto kwa chigwacho.

  • 1 Mbiri 11:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako, atatu mwa atsogoleri 30+ anapita kwa Davide kuthanthwe, kuphanga la Adulamu.+ Pa nthawiyi gulu lankhondo la Afilisiti linali litamanga msasa m’chigwa cha Arefai.+

  • 1 Mbiri 14:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Afilisitiwo anafika ndi kuyamba kufunkha m’chigwa cha Arefai.+

  • Yesaya 17:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Munthu wokolola akamadzadula tirigu m’munda ndipo dzanja lake likamadzakolola ngala za tirigu,+ adzakhala ngati munthu wokunkha ngala za tirigu m’chigwa cha Arefai.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena