Yesaya 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zidzakhala ngati zimene zimachitika wokolola akamadula tirigu mʼmundaKomanso dzanja lake likamakolola ngala za tirigu.Zidzakhala ngati mmene zimakhalira munthu akamakunkha tirigu mʼchigwa cha Arefai.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:5 Yesaya 1, tsa. 196
5 Zidzakhala ngati zimene zimachitika wokolola akamadula tirigu mʼmundaKomanso dzanja lake likamakolola ngala za tirigu.Zidzakhala ngati mmene zimakhalira munthu akamakunkha tirigu mʼchigwa cha Arefai.+