Yesaya 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wokolola akamadzadula tirigu m’munda ndipo dzanja lake likamadzakolola ngala za tirigu,+ adzakhala ngati munthu wokunkha ngala za tirigu m’chigwa cha Arefai.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:5 Yesaya 1, tsa. 196
5 Munthu wokolola akamadzadula tirigu m’munda ndipo dzanja lake likamadzakolola ngala za tirigu,+ adzakhala ngati munthu wokunkha ngala za tirigu m’chigwa cha Arefai.+