Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 15:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kuchokera pamenepo, anapitirira mpaka kuchigwa cha mwana wa Hinomu,+ kumalo otsetsereka otchedwa Yebusi+ kumʼmwera, kutanthauza Yerusalemu.+ Anapitirirabe mpaka pamwamba pa phiri loyangʼanizana ndi chigwa cha Hinomu, limene lili kumadzulo kwa chigwacho. Phirilo lili kumpoto kwa chigwa cha Arefai, kumapeto kwa chigwacho.

  • Yoswa 15:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Malire akumadzulo anali Nyanja Yaikulu*+ ndi gombe lake. Amenewa anali malire a ana a Yuda a mbali zonse motsatira mabanja awo.

  • Yoswa 18:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Maere oyamba anagwera fuko la Benjamini motsatira mabanja awo, ndipo anapatsidwa dera limene linali pakati pa ana a Yuda+ ndi ana a Yosefe.+

  • Yoswa 18:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Malirewo anakafika kumapeto kwa phiri loyangʼanizana ndi chigwa cha Mwana wa Hinomu,+ limene linathera kumpoto kwa chigwa cha Arefai.+ Kenako anatsetserekera kuchigwa cha Hinomu kumʼmwera kwa malo otsetsereka otchedwa Yebusi+ mpaka kukafika ku Eni-rogeli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena