1 Mbiri 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno ana a Amoni anapita kukafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo kuchipata cha mzinda. Ndipo mafumu+ amene anabwera aja anali okhaokha kutchire.
9 Ndiyeno ana a Amoni anapita kukafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo kuchipata cha mzinda. Ndipo mafumu+ amene anabwera aja anali okhaokha kutchire.