1 Mbiri 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno nkhondo imeneyi itatha, panabukanso nkhondo ina ndi Afilisiti+ ku Gezeri.+ Pa nthawi imeneyo Sibekai+ Mhusati anapha Sipa, amene anali mmodzi mwa mbadwa za Arefai,+ moti Afilisiti anagonjetsedwa.
4 Ndiyeno nkhondo imeneyi itatha, panabukanso nkhondo ina ndi Afilisiti+ ku Gezeri.+ Pa nthawi imeneyo Sibekai+ Mhusati anapha Sipa, amene anali mmodzi mwa mbadwa za Arefai,+ moti Afilisiti anagonjetsedwa.