1 Mbiri 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nkhondo imeneyi itatha, panabukanso nkhondo ina ndi Afilisiti ku Gezeri. Pa nthawi imeneyo Sibekai+ wa ku Husa* anapha Sipa, amene anali mbadwa ya Arefai,+ moti Afilisiti anagonjetsedwa.
4 Nkhondo imeneyi itatha, panabukanso nkhondo ina ndi Afilisiti ku Gezeri. Pa nthawi imeneyo Sibekai+ wa ku Husa* anapha Sipa, amene anali mbadwa ya Arefai,+ moti Afilisiti anagonjetsedwa.