1 Mbiri 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamene zimenezi zinali kuchitika, Orinani+ anali akupuntha tirigu. Atatembenuka anaona mngelo, ndipo ana ake anayi amene anali naye limodzi anakabisala.
20 Pamene zimenezi zinali kuchitika, Orinani+ anali akupuntha tirigu. Atatembenuka anaona mngelo, ndipo ana ake anayi amene anali naye limodzi anakabisala.