1 Mbiri 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Davide anali atasiya kupita kumeneko kukafunsira kwa Mulungu, chifukwa anali kuopa+ lupanga la mngelo wa Yehova.
30 Davide anali atasiya kupita kumeneko kukafunsira kwa Mulungu, chifukwa anali kuopa+ lupanga la mngelo wa Yehova.