1 Mbiri 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 wa 6 Amiyeli, wa 7 Isakara, ndipo wa 8 anali Peuletai, pakuti Mulungu anamudalitsa.+