Deuteronomo 28:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Yehova adzachulukitsa chuma chako pa zipatso za mimba yako,+ zipatso za ziweto zako ndi zipatso za m’munda mwako,+ m’dziko limene Yehova analumbirira makolo ako kuti adzakupatsa.+ Salimo 127:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndicho mphoto.+
11 “Yehova adzachulukitsa chuma chako pa zipatso za mimba yako,+ zipatso za ziweto zako ndi zipatso za m’munda mwako,+ m’dziko limene Yehova analumbirira makolo ako kuti adzakupatsa.+