1 Mbiri 27:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Obili Mwisimaeli+ anali kuyang’anira ngamila.+ Yedeya Mmeronoti anali kuyang’anira abulu aakazi.