-
2 Mbiri 22:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Koma Yehosabati+ mwana wamkazi wa mfumu, anaba Yehoasi+ mwana wamwamuna wa Ahaziya, pakati pa ana aamuna a mfumu amene anayenera kuphedwa. Anatenga Yehoasi pamodzi ndi mlezi wake n’kukamubisa m’chipinda chamkati chogona. Yehosabati, mwana wamkazi wa Mfumu Yehoramu,+ mkazi wa wansembe Yehoyada,+ (popeza iye anali mlongo wake wa Ahaziya,) anabisa mwanayo chifukwa choopa Ataliya, ndipo mwanayo sanaphedwe.+
-