-
2 Mbiri 24:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Pa nthawi yoyenera, Alevi+ ankanyamula bokosilo n’kupita nalo kwa mfumu. Iwo akangoona kuti muli ndalama zambiri,+ mlembi+ wa mfumu ndi mtumiki wa wansembe wamkulu ankabwera n’kukhuthula ndalama zimene zinali m’bokosilo, n’kulinyamula kukalibwezeretsa pamalo ake. Ankachita zimenezi tsiku ndi tsiku moti anasonkhetsa ndalama zambiri.
-