Ezara 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno ife tinafunsa akuluakulu amenewo kuti: ‘Kodi ndani wakulamulani kuti mumange nyumbayi ndi kumaliza khoma lamatabwali?’+
9 Ndiyeno ife tinafunsa akuluakulu amenewo kuti: ‘Kodi ndani wakulamulani kuti mumange nyumbayi ndi kumaliza khoma lamatabwali?’+