Ezara 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno tinafunsa akuluakulu awo kuti: ‘Kodi ndi ndani wakulamulani kuti mumange nyumbayi komanso kumaliza ntchitoyi?’*+
9 Ndiyeno tinafunsa akuluakulu awo kuti: ‘Kodi ndi ndani wakulamulani kuti mumange nyumbayi komanso kumaliza ntchitoyi?’*+