Ezara 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli ndinu wolungama+ chifukwa ife tatsala monga anthu opulumuka lero. Taima pamaso panu m’machimo athu,+ ngakhale kuti n’zosatheka kuima pamaso panu chifukwa cha machimo athuwo.”+
15 Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli ndinu wolungama+ chifukwa ife tatsala monga anthu opulumuka lero. Taima pamaso panu m’machimo athu,+ ngakhale kuti n’zosatheka kuima pamaso panu chifukwa cha machimo athuwo.”+