Salimo 130:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Ya, mukanakhala kuti mumayang’anitsitsa zolakwa,+Ndani akanaima pamaso panu, inu Yehova?+ Salimo 143:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musandiimbe mlandu ine mtumiki wanu,+Pakuti palibe aliyense wamoyo amene angakhale wolungama pamaso panu.+
2 Musandiimbe mlandu ine mtumiki wanu,+Pakuti palibe aliyense wamoyo amene angakhale wolungama pamaso panu.+