-
Ezara 10:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Choncho aloleni akalonga+ athu kuti aimire mpingo wonse ndipo anthu onse a m’mizinda yathu amene atenga akazi achilendo, abwere pa nthawi zimene zikhazikitsidwe. Abwere limodzi ndi akulu a mzinda uliwonse ndi oweruza ake, mpaka titathetsa mkwiyo wa Mulungu wathu umene watiyakira pa nkhani imeneyi.”
-