Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 3:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Ndiyeno mfumu inapitiriza kuuza atumiki ake kuti: “Kodi simukudziwa kuti amene wafa leroyu ndi kalonga komanso munthu wamphamvu mu Isiraeli?+

  • Ezara 9:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Zinthu zimenezi zitangotha, akalonga+ anabwera kwa ine n’kundiuza kuti: “Aisiraeli, ansembe ndiponso Alevi sanadzipatule+ kwa anthu a mitundu ina pa nkhani ya zinthu zonyansa+ za anthu a mitundu inawo. Anthu ake ndi Akanani,+ Ahiti,+ Aperezi,+ Ayebusi,+ Aamoni,+ Amowabu,+ Aiguputo+ ndi Aamori.+

  • Ezara 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 ndi kuti aliyense amene sabwera+ potha masiku atatu mogwirizana ndi lamulo la akalonga+ ndi akulu, katundu wake yense alandidwa+ ndipo iyeyo achotsedwa+ pa khamu la anthu amene anachokera ku ukapolo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena