19 Choncho malire a dziko la Akanani anachokera ku Sidoni mpaka ku Gerari+ kufupi ndi Gaza,+ n’kukafika ku Sodomu ndi Gomora+ mpakanso ku Adima+ ndi Zeboyimu,+ kufupi ndi Lasa.
29 Aamaleki+ amakhala ku Negebu.+ Ahiti, Ayebusi+ ndi Aamori+ amakhala kudera lamapiri. Akanani+ amakhala m’mphepete mwa nyanja, ndi m’mphepete mwa mtsinje wa Yorodano.”