Genesis 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma m’badwo wachinayi udzabwerera kuno,+ chifukwa nthawi yoti Aamori alangidwe sinakwane.”+ Oweruza 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Motero anatenga chigawo cha Aamori kuchokera ku Arinoni kukafika ku Yaboki ndiponso kuchokera kuchipululu kukafika ku Yorodano.+
22 Motero anatenga chigawo cha Aamori kuchokera ku Arinoni kukafika ku Yaboki ndiponso kuchokera kuchipululu kukafika ku Yorodano.+