Levitiko 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musachite+ zimene amachita anthu a ku Iguputo kumene munali kukhala, ndipo musakachite+ zimene amachita m’dziko la Kanani, kumene ndikukulowetsani. Musakatsatire mfundo zawo.
3 Musachite+ zimene amachita anthu a ku Iguputo kumene munali kukhala, ndipo musakachite+ zimene amachita m’dziko la Kanani, kumene ndikukulowetsani. Musakatsatire mfundo zawo.