Genesis 19:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero. Deuteronomo 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Muamoni kapena Mmowabu asalowe mumpingo wa Yehova.+ Ana awo asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10, ngakhalenso mpaka kalekale.
38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero.
3 “Muamoni kapena Mmowabu asalowe mumpingo wa Yehova.+ Ana awo asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10, ngakhalenso mpaka kalekale.