Yoswa 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anaitanitsanso Akanani+ okhala kum’mawa ndi kumadzulo, ndiponso Aamori,+ Ahiti,+ Aperezi+ ndi Ayebusi+ okhala kudera lamapiri. Komanso anaitanitsa Ahivi+ omwe anali kukhala m’munsi mwa phiri la Herimoni+ ku Mizipa.+ Yoswa 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.”
3 Anaitanitsanso Akanani+ okhala kum’mawa ndi kumadzulo, ndiponso Aamori,+ Ahiti,+ Aperezi+ ndi Ayebusi+ okhala kudera lamapiri. Komanso anaitanitsa Ahivi+ omwe anali kukhala m’munsi mwa phiri la Herimoni+ ku Mizipa.+
15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.”