Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 19:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Molamulidwa ndi Yehova, anam’patsa mzinda umene anapempha+ wa Timinati-sera,+ m’dera lamapiri la Efuraimu ndipo iye anayamba kumanga mzindawo n’kumakhalamo.

  • Yoswa 24:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Nayenso Eleazara mwana wa Aroni anamwalira.+ Choncho anamuika m’manda m’phiri la Pinihasi mwana wake,+ limene anapatsidwa m’dera lamapiri la Efuraimu.

  • Oweruza 7:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndiyeno Gidiyoni anatumiza amithenga kudera lonse lamapiri la Efuraimu,+ kuti: “Pitani mofulumira ku Beti-bara ndi kumtsinje wa Yorodano, ndipo mukaike amuna m’malo owolokera kuti Amidiyani asadutse.” Choncho, amuna onse a Efuraimu anasonkhana pamodzi ndipo anatseka malo owolokera Yorodano ndi mitsinje yake ing’onoing’ono+ mpaka ku Beti-bara.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena