Yoswa 24:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho anamuika m’manda m’gawo la cholowa chake ku Timinati-sera,+ kudera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi. Oweruza 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo anamuika m’manda ku Timinati-heresi,*+ m’dera limene analandira monga cholowa chake, m’dera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.+
30 Choncho anamuika m’manda m’gawo la cholowa chake ku Timinati-sera,+ kudera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.
9 Ndipo anamuika m’manda ku Timinati-heresi,*+ m’dera limene analandira monga cholowa chake, m’dera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.+