Yoswa 19:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Molamulidwa ndi Yehova, anam’patsa mzinda umene anapempha+ wa Timinati-sera,+ m’dera lamapiri la Efuraimu ndipo iye anayamba kumanga mzindawo n’kumakhalamo. Oweruza 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo anamuika m’manda ku Timinati-heresi,*+ m’dera limene analandira monga cholowa chake, m’dera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.+
50 Molamulidwa ndi Yehova, anam’patsa mzinda umene anapempha+ wa Timinati-sera,+ m’dera lamapiri la Efuraimu ndipo iye anayamba kumanga mzindawo n’kumakhalamo.
9 Ndipo anamuika m’manda ku Timinati-heresi,*+ m’dera limene analandira monga cholowa chake, m’dera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.+