Numeri 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Nadabu ndi Abihu anafa pamaso pa Yehova pamene anapereka kwa Yehova moto wosaloleka+ m’chipululu cha Sinai, ndipo iwo anafa opanda ana. Komabe, Eleazara+ ndi Itamara+ anapitiriza kutumikira monga ansembe limodzi ndi Aroni bambo awo. Numeri 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 M’phirimo, ukamuvule Aroni zovala zake zaunsembe,+ n’kuveka mwana wake Eleazara.+ Aroni akamwalira kumeneko n’kugona ndi makolo ake.”+
4 Koma Nadabu ndi Abihu anafa pamaso pa Yehova pamene anapereka kwa Yehova moto wosaloleka+ m’chipululu cha Sinai, ndipo iwo anafa opanda ana. Komabe, Eleazara+ ndi Itamara+ anapitiriza kutumikira monga ansembe limodzi ndi Aroni bambo awo.
26 M’phirimo, ukamuvule Aroni zovala zake zaunsembe,+ n’kuveka mwana wake Eleazara.+ Aroni akamwalira kumeneko n’kugona ndi makolo ake.”+