Numeri 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Uwu ndiwo utumiki umene mabanja a ana a Gerisoni+ azichita m’chihema chokumanako. Itamara+ mwana wa wansembe Aroni, ndiye aziyang’anira utumiki wawo. Numeri 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ana a Merari anawapatsa ngolo zinayi ndi ng’ombe 8, malinga ndi utumiki wawo+ umene anali kuchita moyang’aniridwa ndi Itamara, mwana wa wansembe Aroni.+
28 Uwu ndiwo utumiki umene mabanja a ana a Gerisoni+ azichita m’chihema chokumanako. Itamara+ mwana wa wansembe Aroni, ndiye aziyang’anira utumiki wawo.
8 Ana a Merari anawapatsa ngolo zinayi ndi ng’ombe 8, malinga ndi utumiki wawo+ umene anali kuchita moyang’aniridwa ndi Itamara, mwana wa wansembe Aroni.+