Numeri 3:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ntchito imene ana a Merari anapatsidwa inali yosamalira mafelemu+ a chihema chopatulika, mipiringidzo yake,+ mizati yake,+ zitsulo zokhazikapo mafelemu ndi mizati, ziwiya zonse+ ndi zina zonse zokhudza utumiki umenewu.+ Numeri 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano uyu ndi katundu amene azinyamula,+ monga gawo la utumiki wawo m’chihema chokumanako: Mafelemu+ a chihema chopatulika, mipiringidzo yake,+ mizati yake,+ ndiponso zitsulo zokhazikapo mizati ndi mafelemu.+
36 Ntchito imene ana a Merari anapatsidwa inali yosamalira mafelemu+ a chihema chopatulika, mipiringidzo yake,+ mizati yake,+ zitsulo zokhazikapo mafelemu ndi mizati, ziwiya zonse+ ndi zina zonse zokhudza utumiki umenewu.+
31 Tsopano uyu ndi katundu amene azinyamula,+ monga gawo la utumiki wawo m’chihema chokumanako: Mafelemu+ a chihema chopatulika, mipiringidzo yake,+ mizati yake,+ ndiponso zitsulo zokhazikapo mizati ndi mafelemu.+