Numeri 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ana a Merari anawapatsa ngolo 4 ndi ngʼombe zamphongo 8, mogwirizana ndi zimene zinkafunika pa ntchito yawo imene ankagwira moyangʼaniridwa ndi Itamara, mwana wa wansembe Aroni.+
8 Ana a Merari anawapatsa ngolo 4 ndi ngʼombe zamphongo 8, mogwirizana ndi zimene zinkafunika pa ntchito yawo imene ankagwira moyangʼaniridwa ndi Itamara, mwana wa wansembe Aroni.+