Numeri 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ana a Merari anawapatsa ngolo zinayi ndi ng’ombe 8, malinga ndi utumiki wawo+ umene anali kuchita moyang’aniridwa ndi Itamara, mwana wa wansembe Aroni.+
8 Ana a Merari anawapatsa ngolo zinayi ndi ng’ombe 8, malinga ndi utumiki wawo+ umene anali kuchita moyang’aniridwa ndi Itamara, mwana wa wansembe Aroni.+