Deuteronomo 4:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Dera limeneli linayambira ku Aroweli+ m’mphepete mwa chigwa* cha Arinoni mpaka kuphiri la Sione, limene ndi phiri la Herimoni,+ Yoswa 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anapatsidwanso dera la Giliyadi, la Agesuri,+ la Amaakati, phiri lonse la Herimoni,+ ndi dera lonse la Basana+ mpaka ku Saleka.+
48 Dera limeneli linayambira ku Aroweli+ m’mphepete mwa chigwa* cha Arinoni mpaka kuphiri la Sione, limene ndi phiri la Herimoni,+
11 Anapatsidwanso dera la Giliyadi, la Agesuri,+ la Amaakati, phiri lonse la Herimoni,+ ndi dera lonse la Basana+ mpaka ku Saleka.+