Deuteronomo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 (Asidoni anali kutcha phiri la Herimoni kuti Sirioni,+ pamene Aamori anali kulitcha kuti Seniri.)+ Yoswa 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anaitanitsanso Akanani+ okhala kum’mawa ndi kumadzulo, ndiponso Aamori,+ Ahiti,+ Aperezi+ ndi Ayebusi+ okhala kudera lamapiri. Komanso anaitanitsa Ahivi+ omwe anali kukhala m’munsi mwa phiri la Herimoni+ ku Mizipa.+
3 Anaitanitsanso Akanani+ okhala kum’mawa ndi kumadzulo, ndiponso Aamori,+ Ahiti,+ Aperezi+ ndi Ayebusi+ okhala kudera lamapiri. Komanso anaitanitsa Ahivi+ omwe anali kukhala m’munsi mwa phiri la Herimoni+ ku Mizipa.+