Nehemiya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mukadzabwerera kwa ine+ ndi kusunga malamulo anga,+ ngakhale anthu omwazikana a mtundu wanu atakhala kumalekezero a kumwamba, ndidzawasonkhanitsa kuchokera kumeneko+ ndi kuwabweretsa+ kumalo amene ndasankha kuikako dzina langa.’+
9 Mukadzabwerera kwa ine+ ndi kusunga malamulo anga,+ ngakhale anthu omwazikana a mtundu wanu atakhala kumalekezero a kumwamba, ndidzawasonkhanitsa kuchokera kumeneko+ ndi kuwabweretsa+ kumalo amene ndasankha kuikako dzina langa.’+