Nehemiya 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Awa ndi anthu a m’chigawo+ amene anatuluka mu ukapolo+ wa anthu omwe Nebukadinezara+ mfumu ya ku Babulo anawatengera ku ukapolo ku Babulo.+ Anthuwa anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense kumzinda wakwawo.+ Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:6 Nsanja ya Olonda,2/15/1986, tsa. 31
6 Awa ndi anthu a m’chigawo+ amene anatuluka mu ukapolo+ wa anthu omwe Nebukadinezara+ mfumu ya ku Babulo anawatengera ku ukapolo ku Babulo.+ Anthuwa anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense kumzinda wakwawo.+